Ekisodo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino ndipo chinali chosula. Choikapo nyalecho chinali chinthu chimodzi ndipo chinali ndi tsinde, thunthu, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+
17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino ndipo chinali chosula. Choikapo nyalecho chinali chinthu chimodzi ndipo chinali ndi tsinde, thunthu, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+