-
Ekisodo 37:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Analikuta ndi golide woyenga bwino pamwamba pake ndi mʼmbali mwake kuzungulira guwalo komanso nyanga zake. Ndipo anapanga mkombero wagolide kuzungulira guwa lonselo.
-