-
Ekisodo 38:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Analipangiranso mphete 4 mʼmakona ake 4 kuti muzilowa ndodo zonyamulira. Mphetezo anazilumikiza pafupi ndi sefa wa zitsulo zakopa.
-