-
Ekisodo 38:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndodozo anazilowetsa mumphetezo mʼmbali mwa guwa kuti zikhale zonyamulira guwalo. Guwa limenelo analipanga ngati bokosi lamatabwa losatseka pansi.
-