-
Ekisodo 38:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Panali zipilala 20 ndi zitsulo 20 zakopa zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.
-