-
Ekisodo 38:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Koma kumbali yakumadzulo, mpanda wa nsaluwo unali mamita 23 mulitali mwake. Kunali zipilala 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.
-