Ekisodo 38:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo siliva wa anthu amene anawerengedwa mʼgulu la Isiraeli, anali matalente 100 ndi masekeli 1,775 potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.*
25 Ndipo siliva wa anthu amene anawerengedwa mʼgulu la Isiraeli, anali matalente 100 ndi masekeli 1,775 potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.*