Ekisodo 38:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Popanga zitsulo za malo oyera zokhazikapo mafelemu ndi zitsulo zokhazikapo zipilala za makatani anagwiritsa ntchito matalente 100. Popanga zitsulo 100 anagwiritsa ntchito matalente 100, talente imodzi anapangira chitsulo chimodzi.+
27 Popanga zitsulo za malo oyera zokhazikapo mafelemu ndi zitsulo zokhazikapo zipilala za makatani anagwiritsa ntchito matalente 100. Popanga zitsulo 100 anagwiritsa ntchito matalente 100, talente imodzi anapangira chitsulo chimodzi.+