Ekisodo 38:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anapangiranso zitsulo zokhazikapo zipilala za mpanda wa bwalo lonse, zitsulo zokhazikapo zipilala zapakhomo la bwalolo, zikhomo zonse za chihema ndi zikhomo zonse za bwalo.+
31 Anapangiranso zitsulo zokhazikapo zipilala za mpanda wa bwalo lonse, zitsulo zokhazikapo zipilala zapakhomo la bwalolo, zikhomo zonse za chihema ndi zikhomo zonse za bwalo.+