-
Ekisodo 39:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Kenako, mumpendero wamʼmunsi wa malaya odula manjawo anapangamo zinthu zooneka ngati makangaza za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri wopota pamodzi.
-