Ekisodo 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142
30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+