Ekisodo 39:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 guwa lansembe lakopa,+ sefa wake wa zitsulo zakopa, ndodo zake zonyamulira,+ ziwiya zonse+ zogwiritsa ntchito paguwalo, beseni losambira ndi choikapo chake.+
39 guwa lansembe lakopa,+ sefa wake wa zitsulo zakopa, ndodo zake zonyamulira,+ ziwiya zonse+ zogwiritsa ntchito paguwalo, beseni losambira ndi choikapo chake.+