Ekisodo 39:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anabweretsanso nsalu zotchingira bwalo, zipilala ndi zitsulo zokhazikapo zipilalazo,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo, zikhomo za bwalo ndi zingwe zake,+ ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wapachihema, kapena kuti chihema chokumanako,
40 Anabweretsanso nsalu zotchingira bwalo, zipilala ndi zitsulo zokhazikapo zipilalazo,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo, zikhomo za bwalo ndi zingwe zake,+ ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wapachihema, kapena kuti chihema chokumanako,