Ekisodo 39:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 zovala zolukidwa bwino zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni wansembe+ ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.
41 zovala zolukidwa bwino zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni wansembe+ ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.