Ekisodo 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene Mose ankamanga chihemacho, anayala pansi zitsulo zake+ nʼkukhazikamo mafelemu.+ Ndiyeno analowetsa ndodo zake+ nʼkuimika zipilala pamalo ake.
18 Pamene Mose ankamanga chihemacho, anayala pansi zitsulo zake+ nʼkukhazikamo mafelemu.+ Ndiyeno analowetsa ndodo zake+ nʼkuimika zipilala pamalo ake.