Ekisodo 40:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anaika mkate+ pamalo ake pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.