Levitiko 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno ana a Aroni ansembe, aziyala nyama yoduladulayo+ pankhuni zimene zili pamoto wapaguwa lansembepo. Aziyala nyamayo pamodzi ndi mutu ndiponso mafuta.*
8 Ndiyeno ana a Aroni ansembe, aziyala nyama yoduladulayo+ pankhuni zimene zili pamoto wapaguwa lansembepo. Aziyala nyamayo pamodzi ndi mutu ndiponso mafuta.*