Levitiko 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako nyamayo aziiduladula ndipo azichotsa mafuta ake* ndi mutu wake. Akatero wansembe aziyala nyama yoduladulayo pankhuni zimene zili pamoto wapaguwa lansembe.
12 Kenako nyamayo aziiduladula ndipo azichotsa mafuta ake* ndi mutu wake. Akatero wansembe aziyala nyama yoduladulayo pankhuni zimene zili pamoto wapaguwa lansembe.