Levitiko 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamapereka kwa Yehova nsembe yambewu ya zipatso zoyambirira kucha, muzipereka tirigu watsopano* wokazinga pamoto, wosinja kuti akhale nsembe yambewu ya zipatso zanu zoyambirira kucha.+
14 Mukamapereka kwa Yehova nsembe yambewu ya zipatso zoyambirira kucha, muzipereka tirigu watsopano* wokazinga pamoto, wosinja kuti akhale nsembe yambewu ya zipatso zanu zoyambirira kucha.+