-
Levitiko 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako azichotsa mafuta onse a ngʼombe ya nsembe yamachimo, kuphatikizapo mafuta okuta matumbo ndi mafuta onse apamatumbo.
-