Levitiko 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zinthu zimenezi zizikhala zofanana ndi zomwe azichotsa pa ngʼombe ya nsembe yamgwirizano.+ Ndipo wansembe aziziwotcha paguwa lansembe zopsereza.
10 Zinthu zimenezi zizikhala zofanana ndi zomwe azichotsa pa ngʼombe ya nsembe yamgwirizano.+ Ndipo wansembe aziziwotcha paguwa lansembe zopsereza.