Levitiko 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wansembe aziviika chala chake mʼmagaziwo nʼkudontheza pansi ena mwa magaziwo maulendo 7 pamaso pa Yehova, patsogolo pa katani.+
17 Wansembe aziviika chala chake mʼmagaziwo nʼkudontheza pansi ena mwa magaziwo maulendo 7 pamaso pa Yehova, patsogolo pa katani.+