Levitiko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Azitenga ngʼombeyo nʼkupita nayo kunja kwa msasa ndipo aziiwotcha ngati mmene anawotchera ngʼombe yoyamba ija.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo ya mpingo wonse.+
21 Azitenga ngʼombeyo nʼkupita nayo kunja kwa msasa ndipo aziiwotcha ngati mmene anawotchera ngʼombe yoyamba ija.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo ya mpingo wonse.+