Levitiko 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akatero aziika dzanja lake pamutu pa nyama ya nsembe yamachimoyo ndipo azipha nyamayo pamalo ophera nyama ya nsembe yopsereza aja.+
29 Akatero aziika dzanja lake pamutu pa nyama ya nsembe yamachimoyo ndipo azipha nyamayo pamalo ophera nyama ya nsembe yopsereza aja.+