Levitiko 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nyamayo ndi chala chake nʼkuwapaka panyanga za guwa lansembe zopsereza.+ Magazi ena onse a nkhosayo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza.
34 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nyamayo ndi chala chake nʼkuwapaka panyanga za guwa lansembe zopsereza.+ Magazi ena onse a nkhosayo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza.