Levitiko 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno azivula zovalazo+ nʼkuvala zina. Akatero azitenga phulusalo nʼkupita nalo kumalo oyera, kunja kwa msasa.+
11 Ndiyeno azivula zovalazo+ nʼkuvala zina. Akatero azitenga phulusalo nʼkupita nalo kumalo oyera, kunja kwa msasa.+