Levitiko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pophika, musaikemo zofufumitsa zilizonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zowotcha pamoto.+ Zimenezi nʼzopatulika koposa+ mofanana ndi nsembe yamachimo komanso nsembe yakupalamula.
17 Pophika, musaikemo zofufumitsa zilizonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zowotcha pamoto.+ Zimenezi nʼzopatulika koposa+ mofanana ndi nsembe yamachimo komanso nsembe yakupalamula.