-
Levitiko 6:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera, ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala, chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.
-