Levitiko 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 impso ziwiri zimene zili pafupi ndi chiuno komanso mafuta okuta impsozo. Azichotsanso mafuta apachiwindi pamodzi ndi impsozo.+
4 impso ziwiri zimene zili pafupi ndi chiuno komanso mafuta okuta impsozo. Azichotsanso mafuta apachiwindi pamodzi ndi impsozo.+