Levitiko 7:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Limeneli linali gawo la Aroni ndi ana ake monga ansembe. Gawoli linali lochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, malinga ndi zimene anawalamula pa tsiku limene anaperekedwa kuti atumikire monga ansembe a Yehova.+
35 Limeneli linali gawo la Aroni ndi ana ake monga ansembe. Gawoli linali lochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, malinga ndi zimene anawalamula pa tsiku limene anaperekedwa kuti atumikire monga ansembe a Yehova.+