Levitiko 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatero anatenga mafuta a nkhosayo, mchira wa mafuta, mafuta onse okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wakumanja.+
25 Atatero anatenga mafuta a nkhosayo, mchira wa mafuta, mafuta onse okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wakumanja.+