Levitiko 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Mose anazitenga mʼmanja mwawo nʼkuziwotcha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza. Zinthu zimenezi zinali nsembe yowaikira kuti akhale ansembe, yakafungo kosangalatsa.* Inali nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.
28 Kenako Mose anazitenga mʼmanja mwawo nʼkuziwotcha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza. Zinthu zimenezi zinali nsembe yowaikira kuti akhale ansembe, yakafungo kosangalatsa.* Inali nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.