-
Levitiko 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Aisiraeli uwauze kuti, ‘Tengani mbuzi yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo. Mutengenso mwana wa ngʼombe ndi nkhosa yaingʼono yamphongo, zonsezi zikhale za chaka chimodzi, zopanda chilema, kuti zikhale nsembe yopsereza.
-