Levitiko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense wonyamula chilichonse mwa zamoyo zimenezi chitafa, azichapa zovala zake,+ ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
25 Aliyense wonyamula chilichonse mwa zamoyo zimenezi chitafa, azichapa zovala zake,+ ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.