Levitiko 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wonyamula iliyonse ya nyama zimenezi itafa, azichapa zovala zake+ ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Nyama zimenezi ndi zodetsedwa kwa inu.
28 Munthu wonyamula iliyonse ya nyama zimenezi itafa, azichapa zovala zake+ ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Nyama zimenezi ndi zodetsedwa kwa inu.