Levitiko 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Musamadye chamoyo chilichonse chokwawa, chamoyo chilichonse chimene chimayenda ndi miyendo yonse 4 kapena zamoyo zonse zimene zimapezeka zambiri padziko lapansi, zokhala ndi miyendo yambiri, chifukwa zimenezi ndi zonyansa.+
42 Musamadye chamoyo chilichonse chokwawa, chamoyo chilichonse chimene chimayenda ndi miyendo yonse 4 kapena zamoyo zonse zimene zimapezeka zambiri padziko lapansi, zokhala ndi miyendo yambiri, chifukwa zimenezi ndi zonyansa.+