-
Levitiko 12:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Akabereka mwana wamkazi, azikhala wodetsedwa kwa masiku 14 ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba. Mkaziyo azipitiriza kudziyeretsa ku magazi ake kwa masiku enanso 66.
-