-
Levitiko 13:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno wansembe azionanso munthuyo pa tsiku la 7, ndipo ngati nthendayo ikuoneka kuti yatha, moti sinafalikire pakhungu, wansembe azimuika munthuyo kwayekha kwa masiku enanso 7.
-