Levitiko 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wansembe azionanso munthuyo kachiwiri pa tsiku la 7. Ngati nthendayo yatheratu ndipo sinafalikire pakhungu, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Inangokhala nkhanambo basi. Kenako munthuyo azichapa zovala zake nʼkukhala woyera.
6 Wansembe azionanso munthuyo kachiwiri pa tsiku la 7. Ngati nthendayo yatheratu ndipo sinafalikire pakhungu, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Inangokhala nkhanambo basi. Kenako munthuyo azichapa zovala zake nʼkukhala woyera.