Levitiko 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wansembe azionanso munthuyo ndipo ngati nkhanambo yake yafalikira pakhungu, wansembeyo azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limenelo ndi khate.+
8 Wansembe azionanso munthuyo ndipo ngati nkhanambo yake yafalikira pakhungu, wansembeyo azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limenelo ndi khate.+