Levitiko 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma wansembe akachiona nʼkupeza kuti palibe cheya choyera ndipo sichinayambire mkati mwa khungu komanso chikuoneka kuti chikutha, wansembe azimuika kwayekha kwa masiku 7.+
21 Koma wansembe akachiona nʼkupeza kuti palibe cheya choyera ndipo sichinayambire mkati mwa khungu komanso chikuoneka kuti chikutha, wansembe azimuika kwayekha kwa masiku 7.+