-
Levitiko 13:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 wansembe aziona balalo. Ngati cheya cha pamalopo chasanduka choyera ndipo balalo likuoneka lozama kuposa khungu, limenelo ndi khate. Latuluka pabala, ndipo wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate.
-