Levitiko 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma ngati wansembe waona balalo, nʼkupeza kuti palibe cheya choyera ndipo balalo si lozama kuposa khungu komanso likutha, wansembe azimuika kwayekha kwa masiku 7.+
26 Koma ngati wansembe waona balalo, nʼkupeza kuti palibe cheya choyera ndipo balalo si lozama kuposa khungu komanso likutha, wansembe azimuika kwayekha kwa masiku 7.+