-
Levitiko 13:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Wansembe aziona munthuyo pa tsiku la 7. Ngati nthendayo yafalikiradi pakhungu, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate.
-