-
Levitiko 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma ngati chikangacho chili pamalo amodzi ndipo sichinafalikire pakhungu komanso chikutha, kumeneko ndi kutupa kwa bala. Wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera chifukwa kumeneko ndi kutukusira kwa bala.
-