30 wansembe aziona nthendayo.+ Ngati pamalopo pakuoneka kuti nthendayo yalowa mkati mwa khungu, komanso tsitsi lachita chikasu ndipo lili patalipatali, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya pamutu ndi ndevu. Ndi khate lakumutu kapena kuchibwano.