-
Levitiko 13:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Pa tsiku la 7 wansembe azionanso nthendayo. Ngati nthenda yapamutu ndi yapandevu sinafalikire pakhungu, ndipo zikuoneka kuti nthendayo sinalowe mkati mwa khungu, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera. Akatero munthuyo azichapa zovala zake nʼkukhala woyera.
-