-
Levitiko 13:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Koma ngati padazi lake kapena pamphumi pake patuluka chilonda chotuwa mofiirira, limenelo ndi khate, latuluka pamutu pake kapena pamphumi pake.
-