Levitiko 13:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 kaya ili mulitali kapena mulifupi* mwa chovala chansalu kapena chaubweya wa nkhosa, kapenanso pachikopa kapena pa chilichonse chopangidwa ndi chikopa,
48 kaya ili mulitali kapena mulifupi* mwa chovala chansalu kapena chaubweya wa nkhosa, kapenanso pachikopa kapena pa chilichonse chopangidwa ndi chikopa,