-
Levitiko 13:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Aziwotcha chovalacho, nsalu ya ubweya wa nkhosa kapena nsalu ina iliyonse, kapena zilizonse zopangidwa ndi chikopa, zimene zagwidwa ndi nthenda ya khateyo, chifukwa khate limenelo ndi loopsa. Ziziwotchedwa pamoto.
-